1 Akorinto 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe, Khristu anaukitsidwa nʼkukhala ngati chipatso choyambirira cha amene akugona mu imfa.+