Aefeso 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza kuchokera pansi pa mtima, ngati mmene mumachitira ndi Khristu. Akolose 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu akapolo, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu+ pa zinthu zonse, osati pokhapokha pamene akukuonani pongofuna kusangalatsa anthu,* koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.* 1 Timoteyo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu onse amene ndi akapolo aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwalemekeza ndi mtima wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndiponso zimene amatiphunzitsa zisanyozedwe.+ Tito 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akapolo azigonjera ambuye awo pa zinthu zonse+ ndipo aziwakondweretsa. Asamatsutsane nawo
5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza kuchokera pansi pa mtima, ngati mmene mumachitira ndi Khristu.
22 Inu akapolo, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu+ pa zinthu zonse, osati pokhapokha pamene akukuonani pongofuna kusangalatsa anthu,* koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.*
6 Anthu onse amene ndi akapolo aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwalemekeza ndi mtima wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndiponso zimene amatiphunzitsa zisanyozedwe.+