Yesaya 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+
5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+