Yuda 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso angelo amene anasiya utumiki umene Mulungu anawapatsa kumwamba komanso malo amene ankayenera kukhala,+ Mulungu anawamanga ndi maunyolo omwe sangaduke* nʼkuwasunga mumdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+
6 Ndiponso angelo amene anasiya utumiki umene Mulungu anawapatsa kumwamba komanso malo amene ankayenera kukhala,+ Mulungu anawamanga ndi maunyolo omwe sangaduke* nʼkuwasunga mumdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+