-
Aroma 15:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Komabe, ndakulemberani mfundo zina mosapita mʼmbali kuti ndikukumbutseninso. Ndachita zimenezi chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu wandisonyeza.
-