Aroma 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi sukudziwa kuti Mulungu akukusonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ komanso kuleza mtima+ nʼcholinga choti ulape?+
4 Kodi sukudziwa kuti Mulungu akukusonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kusakwiya msanga+ komanso kuleza mtima+ nʼcholinga choti ulape?+