Aroma 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndi amene anafa komanso ndi amene anaukitsidwa. Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ ndipo amatilankhulira mochonderera.+ Aheberi 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho akhoza kupulumutsa anthu amene akupemphera kwa Mulungu mʼdzina lake, chifukwa iye sadzafa ndipo aziwachonderera kwa Mulungu.+
34 ndani adzawatsutsa? Khristu Yesu ndi amene anafa komanso ndi amene anaukitsidwa. Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ ndipo amatilankhulira mochonderera.+
25 Choncho akhoza kupulumutsa anthu amene akupemphera kwa Mulungu mʼdzina lake, chifukwa iye sadzafa ndipo aziwachonderera kwa Mulungu.+