-
1 Yohane 2:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Munthu amene amanena kuti, “Ine ndikumudziwa,” koma nʼkumalephera kusunga malamulo ake ndi wabodza ndipo alibe choonadi mumtima mwake.
-