Yohane 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+ 1 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipotu Mulungu anakuitanani kuti muyende mʼnjira imeneyi. Pajatu ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+
15 Chifukwa ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+
21 Ndipotu Mulungu anakuitanani kuti muyende mʼnjira imeneyi. Pajatu ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+