Yohane 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kuti onse alemekeze Mwana ngati mmene amalemekezera Atate. Aliyense amene salemekeza Mwana salemekezanso Atate amene anamutuma.+ 2 Yohane 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu ankaphunzitsa, ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma Atate ndiponso Mwana, amasangalala ndi munthu amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye ankaphunzitsa.+
23 kuti onse alemekeze Mwana ngati mmene amalemekezera Atate. Aliyense amene salemekeza Mwana salemekezanso Atate amene anamutuma.+
9 Aliyense amene amachita zosemphana ndi zimene Khristu ankaphunzitsa, ndiye kuti akukana Mulungu.+ Koma Atate ndiponso Mwana, amasangalala ndi munthu amene amachita zinthu mogwirizana ndi zimene iye ankaphunzitsa.+