-
Aroma 10:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chifukwa ngati ukulengeza ‘mawu amene ali mʼkamwa mwakowo,’ akuti Yesu ndi Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa, udzapulumuka. 10 Kuti munthu akhale wolungama amayenera kukhala ndi chikhulupiriro mumtima mwake, koma ndi pakamwa pake amalengeza+ poyera chikhulupiriro chake kuti apulumuke.
-