Yohane 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati munthu amandikonda, adzasunga mawu anga+ ndipo Atate wanga adzamukonda komanso tidzapita kwa iwo nʼkukakhala nawo.+ 2 Yohane 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo chikondi chimatanthauza kupitiriza kuyenda motsatira malamulo ake.+ Monga mmene munamvera kuyambira pachiyambi, lamulo lake ndi lakuti nthawi zonse muzisonyeza chikondi.
23 Yesu anamuyankha kuti: “Ngati munthu amandikonda, adzasunga mawu anga+ ndipo Atate wanga adzamukonda komanso tidzapita kwa iwo nʼkukakhala nawo.+
6 Ndipo chikondi chimatanthauza kupitiriza kuyenda motsatira malamulo ake.+ Monga mmene munamvera kuyambira pachiyambi, lamulo lake ndi lakuti nthawi zonse muzisonyeza chikondi.