Aroma 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe ngati mfumu mʼmatupi anu oti akhoza kufawo+ kuti muzitsatira zilakolako zawo.
12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe ngati mfumu mʼmatupi anu oti akhoza kufawo+ kuti muzitsatira zilakolako zawo.