Yohane 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, aliyense amene wamva mawu anga nʼkukhulupirira Mulungu amene anandituma, adzapeza moyo wosatha+ ndipo sadzaweruzidwa koma wachoka ku imfa nʼkuwolokera ku moyo.+ Aroma 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa lamulo la mzimu limene limapatsa moyo mogwirizana ndi Khristu Yesu lakumasulani+ ku lamulo la uchimo ndi la imfa.
24 Ndithudi ndikukuuzani, aliyense amene wamva mawu anga nʼkukhulupirira Mulungu amene anandituma, adzapeza moyo wosatha+ ndipo sadzaweruzidwa koma wachoka ku imfa nʼkuwolokera ku moyo.+
2 Chifukwa lamulo la mzimu limene limapatsa moyo mogwirizana ndi Khristu Yesu lakumasulani+ ku lamulo la uchimo ndi la imfa.