Aheberi 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, tiyeni tizifika kumpando wachifumu wa Mulungu ndipo tizipemphera ndi ufulu wa kulankhula+ kuti atichitire chifundo komanso kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi yoyenera. 1 Yohane 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipotu ife sitikayikira*+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi zimene amafuna, amatimvera.+
16 Choncho, tiyeni tizifika kumpando wachifumu wa Mulungu ndipo tizipemphera ndi ufulu wa kulankhula+ kuti atichitire chifundo komanso kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi yoyenera.
14 Ndipotu ife sitikayikira*+ kuti chilichonse chimene tingamupemphe mogwirizana ndi zimene amafuna, amatimvera.+