Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+