2 Atesalonika 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zoona, kuipa kwa munthu ameneyu, komwe ndi kwachinsinsi, kwayamba kale kugwira ntchito.+ Koma kuipa kumeneku kupitiriza kukhala chinsinsi mpaka amene akumulepheretsa atachoka. 1 Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.
7 Zoona, kuipa kwa munthu ameneyu, komwe ndi kwachinsinsi, kwayamba kale kugwira ntchito.+ Koma kuipa kumeneku kupitiriza kukhala chinsinsi mpaka amene akumulepheretsa atachoka.
18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.