Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Komabe ndikuuza zinthu zimene zinalembedwa mʼbuku la choonadi. Palibe aliyense amene akundithandiza kwambiri pa zinthu zimenezi kupatulapo Mikayeli,+ amene ndi kalonga wanu.”+

  • Danieli 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Pa nthawi imeneyo Mikayeli,*+ kalonga wamkulu+ amene waimirira kuti athandize anthu a mtundu wako,* adzaimirira. Ndiyeno padzafika nthawi yamasautso imene sinakhalepo kuyambira pamene mtundu woyambirira wa anthu unakhalapo kudzafika nthawi imeneyo. Pa nthawi imeneyo anthu a mtundu wako, aliyense amene dzina lake lidzakhala litalembedwa mʼbuku, adzapulumuka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena