1 Timoteyo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ena mwa anthuwa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda, ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa, aphunzirepo kanthu nʼkusiya kunyoza Mulungu.
20 Ena mwa anthuwa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda, ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa, aphunzirepo kanthu nʼkusiya kunyoza Mulungu.