Mateyu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Osangalala ndi anthu achifundo+ chifukwa adzachitiridwa chifundo. Mateyu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti: ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.” Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.
13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti: ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”
13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.