-
Chivumbulutso 21:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho, pogwiritsa ntchito mphamvu ya mzimu, ananditenga nʼkundipititsa kuphiri lalikulu ndi lalitali ndipo anandionetsa mzinda woyera wa Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+ 11 ndipo unali ndi ulemerero wa Mulungu.+ Unkanyezimira ngati mwala wamtengo wapatali kwambiri, ngati mwala wa yasipi wowala mbee! ngati galasi.+
-