-
Yobu 39:9-11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kodi ngʼombe yamphongo yamʼtchire imafunitsitsa kukutumikira?+
Kodi ingagone usiku wonse mʼkhola lako?*
10 Kodi ungamange ngʼombe yamʼtchire ndi zingwe kuti ikulimire mizere,
Kapena kodi ingalole kuti upite nayo kuchigwa kukalima?
11 Kodi ungaikhulupirire chifukwa ili ndi mphamvu zochuluka,
Nʼkuisiya kuti ikugwirire ntchito yako yotopetsa?
-