Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi,+Tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+ Mateyu 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba ndipo mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.+
31 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi,+Tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
29 Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba ndipo mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.+