-
Yesaya 34:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Magulu onse ankhondo akumwamba adzawola,
Ndipo kumwamba kudzapindidwa ngati mpukutu.
Magulu awo onse ankhondo adzafota nʼkugwa,
Ngati mmene masamba ofota amathothokera pamtengo wa mpesa
Ndiponso ngati mmene nkhuyu yonyala imathothokera mumtengo wa mkuyu.
-