Yoweli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzawalankhula asilikali ake mokweza+ chifukwa anthu amumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ndi wamphamvu.Tsiku la Yehova ndi lalikulu komanso lochititsa mantha.+ Ndani angalimbe pa tsiku limeneli?”+
11 Yehova adzawalankhula asilikali ake mokweza+ chifukwa anthu amumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ndi wamphamvu.Tsiku la Yehova ndi lalikulu komanso lochititsa mantha.+ Ndani angalimbe pa tsiku limeneli?”+