Chivumbulutso 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzombelo linauzidwa kuti lisawononge zomera zapadziko lapansi, kapena chilichonse chobiriwira, kapena mtengo uliwonse, koma kuti livulaze anthu okhawo amene alibe chidindo cha Mulungu pachipumi pawo.+
4 Dzombelo linauzidwa kuti lisawononge zomera zapadziko lapansi, kapena chilichonse chobiriwira, kapena mtengo uliwonse, koma kuti livulaze anthu okhawo amene alibe chidindo cha Mulungu pachipumi pawo.+