Yesaya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmasiku otsiriza,Phiri la nyumba ya YehovaLidzakhazikika pamwamba penipeni pa mapiri akuluakulu,+Ndipo lidzakwezedwa kupitirira mapiri angʼonoangʼono.Anthu a mitundu yonse adzapita kumeneko.+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”
2 Mʼmasiku otsiriza,Phiri la nyumba ya YehovaLidzakhazikika pamwamba penipeni pa mapiri akuluakulu,+Ndipo lidzakwezedwa kupitirira mapiri angʼonoangʼono.Anthu a mitundu yonse adzapita kumeneko.+
4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”