Ekisodo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga nʼkukubweretsani kwa ine.+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+
4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga nʼkukubweretsani kwa ine.+
31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu. Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka.Adzayenda koma osatopa.”+