-
Chivumbulutso 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Amene wapambana pankhondo, ndidzamuika kuti akhale mzati mʼkachisi wa Mulungu wanga ndipo sadzachokamonso. Ndidzalemba pachipumi pake dzina la Mulungu wanga+ ndiponso dzina la mzinda wa Mulungu wanga, womwe ndi Yerusalemu Watsopano,+ amene akutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu wanga. Ndidzamulembanso dzina langa latsopano.+
-