Mateyu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni kwa anthu amitundu yonse,+ kenako mapeto adzafika. Maliko 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso choyamba uthenga wabwino ukuyenera kulalikidwa kwa anthu amitundu yonse.+ Machitidwe 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mukadzalandira mzimu woyera, mudzakhala ndi mphamvu.+ Ndipo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero* a dziko lapansi.”+
14 Ndipo uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni kwa anthu amitundu yonse,+ kenako mapeto adzafika.
8 Koma mukadzalandira mzimu woyera, mudzakhala ndi mphamvu.+ Ndipo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero* a dziko lapansi.”+