Chivumbulutso 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngelo wa 5 analiza lipenga lake.+ Ndipo ndinaona nyenyezi imene inagwera padziko lapansi kuchokera kumwamba ija. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi wa dzenje lolowera kuphompho.+
9 Mngelo wa 5 analiza lipenga lake.+ Ndipo ndinaona nyenyezi imene inagwera padziko lapansi kuchokera kumwamba ija. Nyenyeziyo inapatsidwa kiyi wa dzenje lolowera kuphompho.+