-
Afilipi 3:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Cholinga changa nʼchoti ndimudziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu za amene anamuukitsa kwa akufa.+ Ndikufunanso kuti ndivutike ngati mmene iye anavutikira,+ mpaka kulolera kufa ngati mmene iye anafera.+ 11 Ndachita zimenezi kuti ngati nʼkotheka ndidzapeze mwayi wodzauka kwa akufa pa kuuka koyamba.+
-