1 Akorinto 15:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma matupi oti akhoza kuwonongekawa akadzakhala oti sangawonongeke komanso matupi oti angafewa akadzasintha nʼkukhala oti sangafe, zimene Malemba amanena zidzakwaniritsidwa, zakuti: “Imfa yamezedwa* kwamuyaya.”+
54 Koma matupi oti akhoza kuwonongekawa akadzakhala oti sangawonongeke komanso matupi oti angafewa akadzasintha nʼkukhala oti sangafe, zimene Malemba amanena zidzakwaniritsidwa, zakuti: “Imfa yamezedwa* kwamuyaya.”+