-
Ekisodo 32:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Komabe Yehova anauza Mose kuti: “Amene wandichimwira ndi amene ndimufufute mʼbuku langa.
-
-
Danieli 12:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 “Pa nthawi imeneyo Mikayeli,*+ kalonga wamkulu+ amene waimirira kuti athandize anthu a mtundu wako,* adzaimirira. Ndiyeno padzafika nthawi yamasautso imene sinakhalepo kuyambira pamene mtundu woyambirira wa anthu unakhalapo kudzafika nthawi imeneyo. Pa nthawi imeneyo anthu a mtundu wako, aliyense amene dzina lake lidzakhala litalembedwa mʼbuku, adzapulumuka.+
-