Yohane 5:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa nthawi ikubwera imene onse amene ali mʼmanda achikumbutso adzamva mawu ake+ 29 ndipo adzatuluka. Amene ankachita zabwino adzauka kuti alandire moyo ndipo amene ankachita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+