Chivumbulutso 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha.
12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha.