1 Mafumu 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ngati kuti kuyenda mʼmachimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati kunali kosakwanira, Ahabu anakwatira Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kutumikira Baala+ nʼkumamugwadira. 2 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehoramu atangoona Yehu, anamʼfunsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji pali uhule wa Yezebeli+ mayi ako ndi zamatsenga zake zambirimbiri?”+
31 Ngati kuti kuyenda mʼmachimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati kunali kosakwanira, Ahabu anakwatira Yezebeli+ mwana wa Etibaala mfumu ya Asidoni,+ ndipo anayamba kutumikira Baala+ nʼkumamugwadira.
22 Yehoramu atangoona Yehu, anamʼfunsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji pali uhule wa Yezebeli+ mayi ako ndi zamatsenga zake zambirimbiri?”+