Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 18
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Machitidwe

      • Utumiki wa Paulo ku Korinto (1-17)

      • Anabwerera ku Antiokeya wa ku Siriya (18-22)

      • Paulo anachoka ku Galatiya ndi ku Fulugiya (23)

      • Apolo, yemwe ankalankhula mwaluso, anathandizidwa (24-28)

Machitidwe 18:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 148

Machitidwe 18:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:24, 26; 1Ak 16:19; 2Ti 4:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 137

    Galamukani!,

    4/2011, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2003, ptsa. 19-20

    12/15/1996, tsa. 22

    6/15/1990, ptsa. 18-19

    Mawu a Mulungu, tsa. 62

Machitidwe 18:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 20:34; 1Ak 4:11, 12; 9:15; 1At 2:9; 2At 3:8, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 148-150

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2012, tsa. 15

    3/1/2009, ptsa. 26-27

    11/15/2003, ptsa. 19-20

    12/15/1996, ptsa. 22-23

    12/1/1992, ptsa. 28-29

    6/15/1990, ptsa. 18-19

    11/15/1986, ptsa. 29-30

Machitidwe 18:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 4:23
  • +Mac 17:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/1999, tsa. 15

Machitidwe 18:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:27; 17:14
  • +Mac 16:1, 2; 1At 3:6
  • +Mac 17:2, 3; 28:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Utumiki wa Ufumu,

    4/2001, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1991, tsa. 28

Machitidwe 18:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:14
  • +Eze 33:4
  • +Mac 20:26
  • +Mac 13:46; 28:28; Aro 1:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, ptsa. 21-22

Machitidwe 18:7

Mawu a M'munsi

  • *

    Kutanthauza kusunagoge.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, ptsa. 18-19

Machitidwe 18:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

Machitidwe 18:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152-153

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/1997, tsa. 11

Machitidwe 18:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152-153

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/1997, tsa. 11

Machitidwe 18:12

Mawu a M'munsi

  • *

    Bwanamkubwa wachigawo cha Roma. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152-153

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/2012, tsa. 23

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 153

Machitidwe 18:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 153

Machitidwe 18:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 23:29; 25:19

Machitidwe 18:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 155

Machitidwe 18:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 153

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2008, tsa. 32

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 16:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152, 154

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2008, tsa. 32

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 17:2

Machitidwe 18:21

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160

Machitidwe 18:22

Mawu a M'munsi

  • *

    Zikuoneka kuti anapita ku Yerusalemu.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:36

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 154

Machitidwe 18:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:6
  • +Mac 14:21, 22; 15:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160

Machitidwe 18:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:1; 1Ak 1:12; 3:5, 6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, ptsa. 20-21

Machitidwe 18:25

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “analangizidwa ndi mawu apakamwa.”

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2010, tsa. 11

    10/1/1996, ptsa. 20-21

Machitidwe 18:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 16:3; 1Ak 16:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 159

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2010, tsa. 11

    11/15/2003, ptsa. 18-19

    10/1/1996, tsa. 21

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, tsa. 21

Machitidwe 18:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 18:15; Sl 16:10; Yes 7:14; Mik 5:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, ptsa. 21-22

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 18:2Mac 18:24, 26; 1Ak 16:19; 2Ti 4:19
Mac. 18:3Mac 20:34; 1Ak 4:11, 12; 9:15; 1At 2:9; 2At 3:8, 10
Mac. 18:4Mt 4:23
Mac. 18:4Mac 17:2
Mac. 18:5Mac 15:27; 17:14
Mac. 18:5Mac 16:1, 2; 1At 3:6
Mac. 18:5Mac 17:2, 3; 28:23
Mac. 18:6Mt 10:14
Mac. 18:6Eze 33:4
Mac. 18:6Mac 20:26
Mac. 18:6Mac 13:46; 28:28; Aro 1:16
Mac. 18:81Ak 1:14
Mac. 18:10Mt 28:20
Mac. 18:15Mac 23:29; 25:19
Mac. 18:171Ak 1:1
Mac. 18:18Aro 16:1
Mac. 18:19Mac 17:2
Mac. 18:22Mac 15:36
Mac. 18:23Mac 16:6
Mac. 18:23Mac 14:21, 22; 15:32
Mac. 18:24Mac 19:1; 1Ak 1:12; 3:5, 6
Mac. 18:26Aro 16:3; 1Ak 16:19
Mac. 18:28De 18:15; Sl 16:10; Yes 7:14; Mik 5:2
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 18:1-28

Machitidwe a Atumwi

18 Kenako Paulo anachoka ku Atene nʼkupita ku Korinto. 2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ wa ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisila, anali atangofika kumene kuchokera ku Italy, chifukwa Kalaudiyo anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kunyumba kwawo. 3 Popeza ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwirira ntchito limodzi,+ chifukwa onse anali opanga matenti. 4 Paulo ankakamba nkhani mʼsunagoge+ tsiku la sabata lililonse+ ndipo ankakopa Ayuda ndi Agiriki.

5 Sila+ ndi Timoteyo+ atafika kuchokera ku Makedoniya, Paulo anatanganidwa kwambiri ndi ntchito yolalikira mawu a Mulungu. Iye ankachitira umboni kwa Ayuda ndiponso kuwatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+ 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndiponso kumunyoza, iye anakutumula zovala zake+ nʼkuwauza kuti: “Magazi anu akhale pamutu panu.+ Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira panopa ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+ 7 Zitatero, iye anachoka kumeneko* nʼkupita kunyumba ya munthu wina dzina lake Titiyo Yusito. Munthuyu anali wolambira Mulungu ndipo nyumba yake inali moyandikana ndi sunagoge. 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa. 9 Komanso usiku, Ambuye anauza Paulo mʼmasomphenya kuti: “Usaope, pitiriza kulankhula. Usakhale chete, 10 chifukwa ine ndili nawe.+ Palibe munthu amene adzakukhudze nʼkukuvulaza, popeza ndili ndi anthu ambiri mumzindawu.” 11 Choncho anakhala kumeneko chaka ndi miyezi 6, akuwaphunzitsa mawu a Mulungu.

12 Pamene Galiyo anali bwanamkubwa* wa Akaya, Ayuda ananyamuka mogwirizana nʼkuukira Paulo ndipo anamutengera kumpando woweruzira milandu. 13 Kumeneko iwo anati: “Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu mʼnjira yosemphana ndi chilamulo.” 14 Koma pamene Paulo ankati azitsegula pakamwa, Galiyo anauza Ayudawo kuti: “Ayuda inu, chikanakhala cholakwa china kapena mlandu waukulu, ndithu ndikanaleza mtima nʼkukumvetserani. 15 Koma ngati nkhani yake ili yokhudza mikangano pa mawu, mayina ndi chilamulo chanu,+ zimenezo muthane nazo nokha. Ine sindikufuna kuti ndikhale woweruza nkhani zoterezi.” 16 Atatero anawauza kuti achoke kumpando woweruzira milanduwo. 17 Zitatero, onse anagwira Sositene,+ mtsogoleri wa sunagoge nʼkuyamba kumumenya pafupi ndi mpando woweruzira milanduwo. Koma zimenezi sizinamukhudze Galiyo ngakhale pangʼono.

18 Paulo atakhala kumeneko kwa masiku ndithu, anatsanzikana ndi abalewo ndipo anapitiriza ulendo wake wapamadzi kulowera ku Siriya. Pa ulendowu anapita limodzi ndi Purisila ndi Akula. Paulo anameta tsitsi lake ku Kenkereya+ chifukwa cha lonjezo limene anachita. 19 Choncho onse anafika ku Efeso, ndipo anzakewo anawasiya kumeneko. Koma iye yekha analowa mʼsunagoge nʼkuyamba kukambirana ndi Ayuda.+ 20 Ngakhale kuti anamupempha mobwerezabwereza kuti akhale nawo kwa masiku ambiri, iye sanalole. 21 Mʼmalomwake, anatsanzikana nawo nʼkuwauza kuti: “Yehova* akalola ndidzabweranso kudzakuonani.” Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wapanyanja 22 ndipo anafika ku Kaisareya. Kenako anapita* kukapereka moni ku mpingo ndipo pambuyo pake anapita ku Antiokeya.+

23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka nʼkuyamba kuyenda malo osiyanasiyana mʼchigawo cha Galatiya ndi Fulugiya+ ndipo ankalimbikitsa ophunzira onse.+

24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ wa ku Alekizandiriya, amene ankalankhula mwaluso, anafika ku Efeso. Iyeyu ankadziwanso bwino Malemba. 25 Mwamuna ameneyu anaphunzitsidwa* njira ya Yehova.* Iye anali wodzipereka kwambiri chifukwa chakuti anali ndi mzimu woyera, ndipo ankalankhula ndi kuphunzitsa molondola za Yesu. Koma ankangodziwa za ubatizo wa Yohane wokha. 26 Munthu ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Ndiyeno Purisila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga nʼkumufotokozera njira ya Mulungu molondola. 27 Ndiponso, popeza kuti ankafunitsitsa kupita ku Akaya, abalewo analembera ophunzira kumeneko. Anawalimbikitsa kuti amulandire ndi manja awiri. Choncho iye atafika kumeneko, anathandiza kwambiri anthu amene anali atakhulupirira chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu. 28 Chifukwa iye anawatsimikizira Ayuda poyera komanso mwamphamvu kuti anali olakwa, ndipo anagwiritsa ntchito Malemba posonyeza kuti Yesu ndiyedi Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena