Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 18
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Kugwa kwa “Babulo Wamkulu” (1-8)

        • “Tulukani mwa iye anthu anga” (4)

      • Kulirira Babulo amene wagwa (9-19)

      • Kumwamba kudzakhala chisangalalo chifukwa cha kugwa kwa Babulo (20)

      • Babulo adzaponyedwa mʼnyanja ngati mwala (21-24)

Chivumbulutso 18:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 259

Chivumbulutso 18:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Mabaibulo ena amati, “mpweya; mawu ouziridwa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 21:9; Yer 51:8; Chv 14:8
  • +Yes 13:21; Yer 50:39

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 58

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 259-261

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, ptsa. 3-5

    4/15/1989, tsa. 9

Chivumbulutso 18:3

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “mkwiyo wake wa.”

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

  • *

    Kapena kuti, “Amalonda oyendayenda.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:7
  • +Chv 17:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 261-264

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, ptsa. 4-5

Chivumbulutso 18:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 48:20; 52:11; Yer 50:8
  • +Yer 51:6, 45; 2Ak 6:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 16-17

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2006, ptsa. 28-29

    10/1/2005, tsa. 24

    4/15/1999, ptsa. 28-30

    4/15/1989, ptsa. 7-9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

    Galamukani!,

    11/8/1996, ptsa. 8-9

    Mtendere Weniweni, tsa. 32

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 32-35

Chivumbulutso 18:5

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “milandu yake.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:9
  • +Chv 16:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

Chivumbulutso 18:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 50:29; 2At 1:6
  • +Sl 137:8; Yer 50:15
  • +Sl 75:8
  • +Chv 16:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

Chivumbulutso 18:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 47:7-9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

    Yesaya 2, tsa. 119

Chivumbulutso 18:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Le 21:9
  • +Yer 50:34

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

    Yesaya 2, tsa. 119

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1989, tsa. 6

    Mtendere Weniweni, tsa. 32

Chivumbulutso 18:9

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 267

Chivumbulutso 18:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 4:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 267

Chivumbulutso 18:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2009, tsa. 23

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “miyoyo ya anthu.”

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2009, tsa. 23

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 47:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:48
  • +Chv 14:12
  • +De 32:43; Aro 12:19; Chv 6:9, 10; 19:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 268-269

Chivumbulutso 18:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:63, 64

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 269

Chivumbulutso 18:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 269-270

Chivumbulutso 18:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 47:9; Aga 5:19, 20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 269-270

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, ptsa. 6-7

    4/1/1989, tsa. 4

Chivumbulutso 18:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:9, 10; 16:5, 6
  • +Ge 9:6; Yer 51:49

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2006, tsa. 28

    2/1/1990, ptsa. 17-20

    5/15/1989, tsa. 5

    5/1/1989, tsa. 6

    4/15/1989, tsa. 23

    4/1/1989, ptsa. 4-5, 8-9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 270-271

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 18:2Yes 21:9; Yer 51:8; Chv 14:8
Chiv. 18:2Yes 13:21; Yer 50:39
Chiv. 18:3Yer 51:7
Chiv. 18:3Chv 17:1, 2
Chiv. 18:4Yes 48:20; 52:11; Yer 50:8
Chiv. 18:4Yer 51:6, 45; 2Ak 6:17
Chiv. 18:5Yer 51:9
Chiv. 18:5Chv 16:19
Chiv. 18:6Yer 50:29; 2At 1:6
Chiv. 18:6Sl 137:8; Yer 50:15
Chiv. 18:6Sl 75:8
Chiv. 18:6Chv 16:19
Chiv. 18:7Yes 47:7-9
Chiv. 18:8Le 21:9
Chiv. 18:8Yer 50:34
Chiv. 18:10Da 4:30
Chiv. 18:16Chv 17:4
Chiv. 18:19Yes 47:11
Chiv. 18:20Yer 51:48
Chiv. 18:20Chv 14:12
Chiv. 18:20De 32:43; Aro 12:19; Chv 6:9, 10; 19:1, 2
Chiv. 18:21Yer 51:63, 64
Chiv. 18:23Yes 47:9; Aga 5:19, 20
Chiv. 18:24Chv 6:9, 10; 16:5, 6
Chiv. 18:24Ge 9:6; Yer 51:49
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 18:1-24

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

18 Zimenezi zitatha, ndinaona mngelo wina akutsika kuchokera kumwamba ali ndi ulamuliro waukulu ndipo dziko lapansi linawala ndi ulemerero wake. 2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo amene ziwanda zimakhala. Wakhalanso malo amene mzimu uliwonse wonyansa* komanso mbalame iliyonse yonyansa ndi imene imadedwa zimabisala.+ 3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu vinyo wa chilakolako chake cha* chiwerewere.*+ Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye chiwerewere.+ Amalonda* apadziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”

4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+ 5 Chifukwa machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira zochita zake zopanda chilungamo.*+ 6 Mubwezereni zofanana ndi zimene iye anachitira ena.+ Mubwezereni kuwirikiza kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ Mʼkapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho kuwirikiza kawiri.+ 7 Pa muyezo umene anadzipezera ulemerero ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, pa muyezo womwewo mumuzunze ndi kumuliritsa. Chifukwa mumtima mwake akumanena kuti: ‘Ine ndine mfumukazi. Si ine mkazi wamasiye ndipo sindidzalira.’+ 8 Nʼchifukwa chake mʼtsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yake ndi imfa, kulira komanso njala ndipo adzapserera ndi moto+ chifukwa Yehova* Mulungu, amene anamuweruza ndi wamphamvu.+

9 Mafumu a dziko lapansi amene anachita naye chiwerewere* nʼkumasangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa pomumvera chisoni, akadzaona utsi ukufuka chifukwa cha kupsa kwake. 10 Iwo adzaima patali chifukwa cha mantha poona mmene akuzunzikira ndipo adzanena kuti: ‘Zomvetsa chisoni! Zomvetsa chisoni! Iwe mzinda waukulu,+ iwe Babulo mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi lokha, chiweruzo chako chafika!’

11 Komanso amalonda apadziko lapansi adzamulirira ndi kumva chisoni, chifukwa palibenso wina amene angawagule katundu wawo yense. 12 Katundu wawoyo ndi golide, siliva, miyala yamtengo wapatali, ngale, nsalu zabwino kwambiri, nsalu zapepo, nsalu zasilika ndi nsalu zofiira kwambiri. Palibe amene akuwagula chilichonse chopangidwa kuchokera ku mtengo wa fungo labwino, zinthu zosiyanasiyana zopangidwa ndi minyanga, mtengo wapamwamba, kopa, chitsulo ndi mwala wa mabo. 13 Komanso palibe amene akuwagula sinamoni, zonunkhiritsa zochokera ku Indiya, zofukiza, mafuta onunkhira, lubani, vinyo, mafuta a maolivi, ufa wabwino kwambiri, tirigu, ngʼombe, nkhosa, mahatchi, ngolo, akapolo ndiponso anthu ena.* 14 Zoonadi, chipatso chabwino chimene unkachilakalaka chija chakuchokera, ndipo zinthu zako zonse zabwino komanso zokongola zawonongeka ndipo anthu sadzazipezanso.

15 Amalonda amene ankagulitsa zinthu zimenezi, amene analemera chifukwa cha iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona mmene akuzunzikira ndipo adzamulirira ndi kumva chisoni. 16 Iwo azidzati: ‘Zomvetsa chisoni! Zomvetsa chisoni! Iwe mzinda waukulu, umene unkavala zovala zapamwamba, zapepo ndi zofiira kwambiri. Iwe mzinda umene unakongoletsedwa mochititsa chidwi ndi zodzikongoletsera zagolide, mwala wamtengo wapatali ndi ngale.+ 17 Zachisoni, chifukwa mu ola limodzi, chuma chochulukachi chawonongedwa!’

Woyendetsa ngalawa aliyense, munthu aliyense woyenda panyanja, ogwira ntchito mʼngalawa ndi anthu onse amene amayenda panyanja nʼkumachita malonda, anaima patali. 18 Ndipo ataona utsi umene unkafuka chifukwa cha kupsa kwake, anafuula kuti: ‘Ndi mzinda uti umene ungafanane ndi mzinda waukulu umenewu?’ 19 Iwo anathira fumbi pamitu pawo akufuula, kulira ndi kumva chisoni, ndipo anati: ‘Nʼzomvetsa chisoni kuti zimenezi zachitikira mzinda waukuluwu. Anthu onse amene anali ndi ngalawa panyanja analemera chifukwa cha chuma chake. Zatheka bwanji kuti mzindawu uwonongedwe mu ola limodzi.’+

20 Sangalalani kumwambako chifukwa cha zimene zamuchitikira.+ Inunso oyera,+ atumwi ndi aneneri, sangalalani chifukwa Mulungu wamupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+

21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu nʼkuuponya mʼnyanja, ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+ 22 Kuimba kwa oimba pogwiritsa ntchito zeze, kwa oimba zitoliro, kwa oimba malipenga ndi kwa oimba ena sikudzamvekanso mwa iwe. Mwa iwe simudzapezekanso mmisiri wa ntchito iliyonse, komanso phokoso la mphero silidzamvekanso mwa iwe. 23 Kuwala kwa nyale sikudzaunikanso mwa iwe. Mawu a mkwati ndi a mkwatibwi sadzamvekanso mwa iwe, chifukwa amalonda ako anali anthu apamwamba padziko lapansi, ndiponso mitundu yonse ya anthu inasocheretsedwa ndi zochita zako zamizimu.+ 24 Mwa iye munapezeka magazi a aneneri, a oyera,+ ndi a onse amene anaphedwa padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena