Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mboni ziwiri (1-13)

        • Zinanenera kwa masiku 1,260 zitavala ziguduli (3)

        • Zinaphedwa koma sizinaikidwe mʼmanda (7-10)

        • Zinakhalanso ndi moyo patatha masiku atatu ndi hafu (11, 12)

      • Tsoka lachiwiri lapita, tsoka lachitatu likubwera (14)

      • Lipenga la 7 (15-19)

        • Ufumu wa Ambuye wathu ndi wa Khristu wake (15)

        • Amene akuwononga dziko lapansi adzawonongedwa (18)

Chivumbulutso 11:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “ndodo yoyezera.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 40:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, ptsa. 12-13

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2150, 2241

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 161-162

Chivumbulutso 11:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 21:2
  • +Chv 13:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, tsa. 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 162-163

Chivumbulutso 11:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    8/1/1994, tsa. 31

    11/1/1993, ptsa. 9-10

    2/1/1986, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 164

    Ulosi wa Danieli, ptsa. 295-296

Chivumbulutso 11:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zek 4:3, 11
  • +Zek 4:12; Mt 5:14
  • +Zek 4:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 164

Chivumbulutso 11:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    5/15/1997, tsa. 12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 164-166

Chivumbulutso 11:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 4:25
  • +1Mf 17:1; Yak 5:17
  • +Eks 7:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    5/15/1997, tsa. 12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 164-165, 166-167, 208

Chivumbulutso 11:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:17; 13:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2020, tsa. 6

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, tsa. 13

    7/1/1987, tsa. 21

    6/15/1987, ptsa. 15-16

    2/1/1986, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-169

Chivumbulutso 11:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-169

Chivumbulutso 11:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 11:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-169

Chivumbulutso 11:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    2/1/1986, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-168

Chivumbulutso 11:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 37:5, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, tsa. 13

    7/1/1987, tsa. 22

    6/15/1987, tsa. 16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 168-170

Chivumbulutso 11:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 169-170, 199

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1987, tsa. 22

Chivumbulutso 11:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 170-171

Chivumbulutso 11:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158, 171

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 13-14

Chivumbulutso 11:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:6
  • +1Mb 29:11; Sl 22:28; Da 4:17, 34; Chv 12:10
  • +Sl 2:6; Da 7:13, 14; Lu 1:32, 33; 22:28, 29; 2Pe 1:11
  • +Sl 145:13; Da 2:44

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158, 171-172, 176

    Lambirani Mulungu, ptsa. 93-94

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1990, tsa. 19

    1/15/1990, ptsa. 19-20

    4/1/1989, ptsa. 19-20

    12/15/1988, ptsa. 13-14

    Kukambitsirana, tsa. 129

Chivumbulutso 11:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 172-173

Chivumbulutso 11:17

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:4; 16:5
  • +Sl 99:1; Zek 14:9; Chv 19:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 172-173, 176

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1993, ptsa. 25-26

Chivumbulutso 11:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 11:6
  • +Amo 3:7; Ahe 1:1; Yak 5:10
  • +Ge 6:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nkhani Zina, article 55

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/2015, ptsa. 6-7

    9/1/2014, ptsa. 3-4, 6

    5/1/2011, tsa. 8

    3/1/1993, ptsa. 5-6

    4/1/1991, ptsa. 6-7

    7/1/1990, ptsa. 3-4, 5-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 173-176

    Galamukani!,

    11/8/1993, tsa. 32

    2/8/1993, ptsa. 21-26, 27-29

    3/8/1992, ptsa. 20-21

    11/8/1991, ptsa. 12-14

    6/8/1990, tsa. 27

    4/8/1990, tsa. 29

    2/8/1990, tsa. 31

    5/8/1988, ptsa. 11-12

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 137

    Mtendere Weniweni, ptsa. 16-17, 97

Chivumbulutso 11:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 8:1, 6; Ahe 8:1, 2; 9:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 175-176

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 11:1Eze 40:3
Chiv. 11:2Chv 21:2
Chiv. 11:2Chv 13:5
Chiv. 11:4Zek 4:3, 11
Chiv. 11:4Zek 4:12; Mt 5:14
Chiv. 11:4Zek 4:14
Chiv. 11:6Lu 4:25
Chiv. 11:61Mf 17:1; Yak 5:17
Chiv. 11:6Eks 7:19
Chiv. 11:7Chv 12:17; 13:7
Chiv. 11:9Chv 11:11
Chiv. 11:11Eze 37:5, 10
Chiv. 11:14Chv 9:12
Chiv. 11:15Chv 8:6
Chiv. 11:151Mb 29:11; Sl 22:28; Da 4:17, 34; Chv 12:10
Chiv. 11:15Sl 2:6; Da 7:13, 14; Lu 1:32, 33; 22:28, 29; 2Pe 1:11
Chiv. 11:15Sl 145:13; Da 2:44
Chiv. 11:16Chv 4:10
Chiv. 11:17Chv 1:4; 16:5
Chiv. 11:17Sl 99:1; Zek 14:9; Chv 19:6
Chiv. 11:18Ahe 11:6
Chiv. 11:18Amo 3:7; Ahe 1:1; Yak 5:10
Chiv. 11:18Ge 6:11
Chiv. 11:191Mf 8:1, 6; Ahe 8:1, 2; 9:11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 11:1-19

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo*+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Pita ukayeze nyumba yopatulika yapakachisi wa Mulungu, guwa lansembe ndi amene akulambira mmenemo. 2 Koma bwalo limene lili kunja kwa nyumba yopatulika yapakachisi ulisiye, usaliyeze chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina. Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+ 3 Ndiyeno ndidzachititsa kuti mboni zanga ziwiri zinenere kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.” 4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi+ komanso zoikapo nyale ziwiri+ ndipo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+

5 Ngati wina aliyense akufuna kuzivulaza, moto umatuluka mʼkamwa mwawo nʼkupsereza adani awo. Ngati wina angafune kuzivulaza, ayenera kuphedwa mwanjira imeneyi. 6 Mboni zimenezi zili ndi mphamvu yotseka kumwamba+ kuti mvula isagwe+ mʼmasiku onse amene zikunenera. Zilinso ndi mphamvu yosandutsa madzi kuti akhale magazi+ komanso yobweretsa mliri wamtundu uliwonse padziko lapansi maulendo ambirimbiri mmene zikufunira.

7 Zikamaliza kuchitira umboni wawo, chilombo chimene chatuluka muphompho chidzachita nazo nkhondo ndipo chidzagonjetsa mbonizo nʼkuzipha.+ 8 Mitembo yawo idzagona pamsewu waukulu wamumzinda waukulu, umene mophiphiritsa ukutchedwa Sodomu ndi Iguputo, kumenenso Ambuye wawo anaphedwa powapachika pamtengo. 9 Mitundu ya anthu yambiri, mafuko, zilankhulo ndi mayiko, adzayangʼanitsitsa mitembo yawo masiku atatu ndi hafu+ ndipo sadzalola kuti mitemboyo iikidwe mʼmanda. 10 Amene akukhala padziko lapansi adzasangalala ndi kukondwera chifukwa cha imfa yawoyo. Iwo adzatumizirana mphatso chifukwa aneneri awiriwa anazunza amene akukhala padziko lapansi.

11 Masiku atatu ndi hafu aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira ndipo amene anaziona anagwidwa ndi mantha aakulu. 12 Kenako mbonizo zinamva mawu ofuula kuchokera kumwamba akuziuza kuti: “Bwerani kuno.” Ndipo zinakwera kumwamba mumtambo adani awo akuona. 13 Mu ola limenelo, kunachitika chivomerezi chachikulu ndipo gawo limodzi mwa magawo 10 a mzindawo linagwa. Anthu 7,000 anaphedwa ndi chivomerezicho ndipo ena onse anachita mantha nʼkupereka ulemerero kwa Mulungu wakumwamba.

14 Tsoka lachiwiri+ lapita. Koma tsoka lachitatu likubwera mofulumira.

15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+

16 Ndipo akulu 24+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu aja, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi ndipo analambira Mulungu. 17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+ 18 Koma mitundu ya anthu inakwiya ndipo inunso munasonyeza mkwiyo wanu. Ndiye nthawi yoikidwiratu inafika yoti akufa aweruzidwe nʼkupereka mphoto+ kwa akapolo anu aneneri+ komanso kwa oyera ndi amene akuopa dzina lanu, olemekezeka ndi onyozeka omwe. Komanso nthawi yoti muwononge amene akuwononga dziko lapansi.”+

19 Nyumba yopatulika yapakachisi wa Mulungu kumwamba inatsegulidwa ndipo likasa la pangano lake linaonekera lili mʼnyumba yake yopatulika yapakachisi.+ Ndiyeno kunachitika mphezi, kunamveka mawu, kunagunda mabingu, kunachita chivomerezi ndipo kunagwa matalala ambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena