Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 17
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Chiweruzo cha “Babulo Wamkulu” (1-18)

        • Hule lalikulu lakhala pachilombo chofiira kwambiri (1-3)

        • Chilombo chimene ‘chinalipo, panopa kulibe, koma chidzatuluka kuphompho’ (8)

        • Nyanga 10 zidzamenyana ndi Mwanawankhosa (12-14)

        • Nyanga 10 zidzadana ndi hule (16, 17)

Chivumbulutso 17:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1
  • +Yer 51:13; Chv 17:15; 19:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 10-11

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 220

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 235-244

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, ptsa. 5-7

    4/15/1989, ptsa. 7-8

    4/1/1989, tsa. 3

Chivumbulutso 17:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yak 4:4; Chv 18:9
  • +Yer 51:7; Chv 14:8; 18:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 220

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 235-244

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, ptsa. 7-8, 10-12

    4/1/1989, ptsa. 3, 5-6

Chivumbulutso 17:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, tsa. 17

    9/1/1989, tsa. 7

    4/15/1989, ptsa. 12-13

    9/1/1987, tsa. 20

    2/1/1986, tsa. 7

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 240-243

    Galamukani!,

    9/8/1987, tsa. 9

Chivumbulutso 17:4

Mawu a M'munsi

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 16:19
  • +Chv 18:11, 12, 19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-245

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, ptsa. 12-13

    4/1/1989, ptsa. 5-6

Chivumbulutso 17:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 19:2
  • +Chv 18:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2008, tsa. 9

    2/1/1990, tsa. 17

    4/15/1989, ptsa. 12-13

    4/1/1989, tsa. 3

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-244

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 209-210

Chivumbulutso 17:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:9; 18:24; 19:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 243-246

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, tsa. 6

    4/15/1989, tsa. 13

    4/1/1989, ptsa. 8-9

Chivumbulutso 17:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:5
  • +Chv 17:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 246-247

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, ptsa. 13-14

Chivumbulutso 17:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 20:1
  • +Eks 32:32; Sl 69:28; Afi 4:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 247-251

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1988, ptsa. 27-28

    9/1/1987, ptsa. 20, 29

    2/1/1986, tsa. 7

    Galamukani!,

    11/8/1987, tsa. 28

Chivumbulutso 17:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 251-253

Chivumbulutso 17:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 9-10

    Galamukani!,

    5/2011, ptsa. 15-16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 251-253

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1988, tsa. 28

    5/15/1988, ptsa. 24-26

    5/1/1988, tsa. 28

    2/1/1988, tsa. 22

    2/1/1986, ptsa. 5-6

Chivumbulutso 17:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2022, tsa. 5

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 253-254

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1988, tsa. 28

    2/1/1986, tsa. 7

Chivumbulutso 17:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 254-255

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1988, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 17:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 254-255

Chivumbulutso 17:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 1:29; Chv 5:6
  • +Mt 28:18; Mac 2:36; 1Ti 6:15
  • +Chv 19:11, 15
  • +Aro 16:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” tsa. 23

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 19

    6/15/2012, tsa. 18

    1/1/2007, tsa. 27

    2/15/1998, ptsa. 16-17

    10/15/1988, ptsa. 19-20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 254-256, 276

Chivumbulutso 17:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 57:20; Yer 51:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 256

    Galamukani!,

    11/8/1996, ptsa. 5-6

Chivumbulutso 17:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:12
  • +Chv 17:8
  • +Chv 17:7
  • +Le 21:9; Chv 18:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 11-14

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 15

    6/15/2012, tsa. 18

    2/1/2004, tsa. 21

    6/1/1996, tsa. 18

    3/1/1994, tsa. 20

    10/15/1988, ptsa. 16-17

    11/1/1987, tsa. 28

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 223

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 256-258

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 36-37

Chivumbulutso 17:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yos 11:19, 20; Miy 21:1
  • +Chv 17:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 11-14

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, ptsa. 14-15

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2012, tsa. 5

    6/15/2012, tsa. 18

    2/1/2004, tsa. 21

    3/1/1994, tsa. 20

    5/15/1989, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 257-258

    Ulosi wa Danieli, tsa. 282

Chivumbulutso 17:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 220

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 258

    Galamukani!,

    11/8/1996, ptsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, tsa. 4

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 17:1Chv 16:1
Chiv. 17:1Yer 51:13; Chv 17:15; 19:2
Chiv. 17:2Yak 4:4; Chv 18:9
Chiv. 17:2Yer 51:7; Chv 14:8; 18:3
Chiv. 17:4Lu 16:19
Chiv. 17:4Chv 18:11, 12, 19
Chiv. 17:5Chv 19:2
Chiv. 17:5Chv 18:5
Chiv. 17:6Chv 6:9; 18:24; 19:2
Chiv. 17:7Chv 17:5
Chiv. 17:7Chv 17:3
Chiv. 17:8Chv 20:1
Chiv. 17:8Eks 32:32; Sl 69:28; Afi 4:3
Chiv. 17:9Chv 17:7
Chiv. 17:11Chv 17:8
Chiv. 17:14Yoh 1:29; Chv 5:6
Chiv. 17:14Mt 28:18; Mac 2:36; 1Ti 6:15
Chiv. 17:14Chv 19:11, 15
Chiv. 17:14Aro 16:20
Chiv. 17:15Yes 57:20; Yer 51:13
Chiv. 17:16Chv 17:12
Chiv. 17:16Chv 17:8
Chiv. 17:16Chv 17:7
Chiv. 17:16Le 21:9; Chv 18:8
Chiv. 17:17Yos 11:19, 20; Miy 21:1
Chiv. 17:17Chv 17:12
Chiv. 17:18Chv 17:5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 17:1-18

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

17 Mmodzi wa angelo 7 amene anali ndi mbale 7 aja,+ anabwera nʼkundiuza kuti: “Bwera, ndikuonetse chiweruzo cha hule lalikulu limene lakhala pamadzi ambiri,+ 2 limene mafumu a dziko lapansi anachita nalo chiwerewere,*+ ndipo linaledzeretsa anthu amene akukhala padziko lapansi ndi vinyo wa chiwerewere* chake.”+

3 Mu mphamvu ya mzimu, mngeloyo ananditengera kuchipululu. Ndipo ndinaona mkazi atakhala pachilombo chofiira kwambiri, chimene chinali ndi mayina onyoza Mulungu paliponse komanso chinali ndi mitu 7 ndi nyanga 10. 4 Mkaziyo anavala zovala zapepo+ ndi zofiira kwambiri ndipo anadzikongoletsa ndi golide, miyala yamtengo wapatali ndiponso ngale.+ Mʼdzanja lake, anali ndi kapu yagolide yodzaza ndi zonyansa ndi zinthu zodetsedwa zokhudzana ndi chiwerewere* chake. 5 Pachipumi pake panalembedwa dzina lachinsinsi lakuti: “Babulo Wamkulu, mayi wa mahule+ ndiponso mayi wa zonyansa zapadziko lapansi.”+ 6 Ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi a oyera ndiponso magazi a mboni za Yesu.+

Nditamuona, ndinadabwa kwambiri. 7 Ndiye mngelo uja anandifunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukudabwa? Ndikuuza chinsinsi cha mkazi+ ameneyu komanso cha chilombo chimene wakwerapo, chimene chili ndi mitu 7 ndi nyanga 10:+ 8 Chilombo chimene waona, chinalipo, koma panopa kulibe, komabe chatsala pangʼono kutuluka kuphompho,+ ndipo chipita kuchiwonongeko. Anthu amene akukhala padziko lapansi, amene mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa, adzadabwa kwambiri akadzaona kuti chilombocho chinalipo, panopa kulibe, koma chidzakhalaponso.

9 Apa mʼpamene pakufunika kuchenjera ndiponso kukhala ndi nzeru: Mitu 7+ ikuimira mapiri 7, amene mkazi uja wakhala pamwamba pake. 10 Palinso mafumu 7. Mafumu 5 agwa, imodzi ilipo, inayo sinafikebe. Koma ikafika, ikuyenera kudzakhala kanthawi kochepa. 11 Ndipo chilombo chimene chinalipo, koma panopa kulibe,+ ndi chimenenso chili mfumu ya 8, koma yatuluka mwa mafumu 7 aja ndipo ikupita kuchiwonongeko.

12 Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10 amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi. 13 Mafumuwa ali ndi maganizo ofanana, choncho adzapereka mphamvu zawo ndi ulamuliro wawo kwa chilombocho. 14 Iwo adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma chifukwa chakuti iye ndi Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, omwe ndi osankhidwa mwapadera ndiponso okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+

15 Mngelo uja anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, magulu a anthu, mayiko komanso zilankhulo.+ 16 Nyanga 10+ zimene waziona zija komanso chilombo,+ zidzadana ndi hulelo.+ Zidzatenga zinthu zake zonse nʼkulisiya lamaliseche ndipo zidzadya minofu yake nʼkulipsereza ndi moto.+ 17 Chifukwa Mulungu anaika pulani mʼmitima yawo kuti zichite mogwirizana ndi maganizo ake+ komanso kuti zikwaniritse maganizo awo ofanana aja, popereka ufumu wawo kwa chilombo+ mpaka mawu a Mulungu atakwaniritsidwa. 18 Ndipo mkazi+ amene unamuonayo akuimira mzinda waukulu umene ukulamulira mafumu a dziko lapansi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena