Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 13
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Chilombo cha mitu 7 chinatuluka mʼnyanja (1-10)

      • Chilombo cha nyanga ziwiri chinatuluka pansi (11-13)

      • Chifaniziro cha chilombo cha mitu 7 (14, 15)

      • Chizindikiro komanso nambala ya chilombo (16-18)

Chivumbulutso 13:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 11:7; 13:18
  • +Yes 57:20; Chv 21:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, ptsa. 8-11, 14-18

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2004, tsa. 4

    4/1/1989, tsa. 20

    12/15/1988, tsa. 19

    2/1/1986, ptsa. 5-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 186-190

Chivumbulutso 13:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:9
  • +Lu 4:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2022, tsa. 15

    5/2022, tsa. 9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 186-188, 189-190, 227

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2004, tsa. 4

    7/15/1990, tsa. 30

    12/15/1988, tsa. 19

    2/1/1986, ptsa. 5-6

    Kukambitsirana, tsa. 129

Chivumbulutso 13:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 190-191

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 13:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 191-192

Chivumbulutso 13:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 11:2, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192

Chivumbulutso 13:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:25
  • +Chv 12:12

Chivumbulutso 13:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, tsa. 15

    2/1/1986, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192

Chivumbulutso 13:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:5; 21:27
  • +Yes 53:7; Mt 27:50; Chv 5:6, 12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 3

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192

Chivumbulutso 13:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 11:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 192-193

Chivumbulutso 13:10

Mawu a M'munsi

  • *

    Mabaibulo ena amati, “Ngati wina akuyenera kuphedwa ndi lupanga, aphedwe ndi lupanga.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 26:52
  • +Da 7:18; 1Ak 6:2; Chv 20:6
  • +Mt 24:13; Ahe 10:36; 12:3
  • +Chv 2:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 192-193

Chivumbulutso 13:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:13; 20:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, ptsa. 3-4

    4/1/1989, tsa. 20

    5/15/1988, ptsa. 25-26

    2/1/1986, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 193-194

Chivumbulutso 13:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 13:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 193-194

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1986, tsa. 6

Chivumbulutso 13:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, ptsa. 3-4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 193-194

Chivumbulutso 13:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 19:20; 20:4
  • +Chv 13:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 194-195, 240-241

    Galamukani!,

    12/8/1990, tsa. 28

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, tsa. 20

    6/1/1988, ptsa. 25-26

    2/1/1986, ptsa. 6-7

Chivumbulutso 13:15

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “mzimu.”

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 194-195, 240-241

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 19-20

Chivumbulutso 13:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:9, 10; 16:2; 19:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2021, tsa. 18

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2004, ptsa. 6-7

    11/1/1997, ptsa. 15-16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 195-198

Chivumbulutso 13:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:11
  • +Chv 15:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    11/1/1997, ptsa. 15-16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 195-198

Chivumbulutso 13:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 3:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2004, ptsa. 3, 4-7

    12/15/1988, ptsa. 19-20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 195-196

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 13:1Chv 11:7; 13:18
Chiv. 13:1Yes 57:20; Chv 21:1
Chiv. 13:2Chv 12:9
Chiv. 13:2Lu 4:6
Chiv. 13:3Chv 13:14
Chiv. 13:5Chv 11:2, 3
Chiv. 13:6Da 7:25
Chiv. 13:6Chv 12:12
Chiv. 13:7Chv 12:17
Chiv. 13:8Chv 3:5; 21:27
Chiv. 13:8Yes 53:7; Mt 27:50; Chv 5:6, 12
Chiv. 13:9Mt 11:15
Chiv. 13:10Mt 26:52
Chiv. 13:10Da 7:18; 1Ak 6:2; Chv 20:6
Chiv. 13:10Mt 24:13; Ahe 10:36; 12:3
Chiv. 13:10Chv 2:10
Chiv. 13:11Chv 16:13; 20:2
Chiv. 13:12Chv 13:1
Chiv. 13:12Chv 13:3
Chiv. 13:14Chv 19:20; 20:4
Chiv. 13:14Chv 13:3
Chiv. 13:16Chv 14:9, 10; 16:2; 19:20
Chiv. 13:17Chv 14:11
Chiv. 13:17Chv 15:2
Chiv. 13:18Da 3:1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 13:1-18

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

13 Ndiyeno chinjokacho chinangoima pamchenga wamʼmbali mwa nyanja.

Kenako ndinaona chilombo+ chikutuluka mʼnyanja.+ Chinali ndi nyanga 10 ndi mitu 7. Panyanga yake iliyonse panali chisoti chachifumu. Koma pamitu yake panali mayina onyoza Mulungu. 2 Chilombo chimene ndinaonacho chinali ngati kambuku koma mapazi ake anali ngati a chimbalangondo ndipo pakamwa pake panali ngati pa mkango. Chinjoka chija+ chinapatsa chilombocho mphamvu yake, mpando wake wachifumu komanso ulamuliro waukulu.+

3 Ndinaona kuti mutu wake umodzi unkaoneka kuti unali utavulazidwa kwambiri. Koma balalo linapola+ ngakhale kuti chikanatha kufa nalo ndipo dziko lonse lapansi linatsatira chilombocho chifukwa chochita nacho chidwi. 4 Iwo analambira chinjoka chija chifukwa chinapereka ulamuliro kwa chilombo. Ndipo analambira chilombocho ndi mawu akuti: “Ndi ndani ali ngati chilombo ndipo ndi ndani angamenyane nacho?” 5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula ndi zonyoza Mulungu. Chinapatsidwanso mphamvu yochita zimene chikufuna kwa miyezi 42.+ 6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake nʼkumanyoza+ Mulungu. Chinkanyoza dzina lake, malo ake okhala komanso amene akukhala kumwamba.+ 7 Chinaloledwa kumenyana ndi oyerawo nʼkuwagonjetsa.+ Chinapatsidwanso ulamuliro pa anthu a fuko lililonse, mtundu uliwonse, chilankhulo chilichonse ndi dziko lililonse. 8 Anthu amene akukhala padziko lapansi adzachilambira. Kuchokera pamene dziko linakhazikitsidwa, anthu amenewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ wa Mwanawankhosa amene anaphedwa.+

9 Aliyense amene ali ndi makutu amve.+ 10 Ngati wina akuyenera kutengedwa kupita ku ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko. Aliyense wopha munthu ndi lupanga, nayenso adzaphedwa ndi lupanga.*+ Apa mʼpamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+

11 Kenako ndinaona chilombo china chikutuluka pansi pa dziko lapansi. Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+ 12 Chilombocho chinalamulira ndi mphamvu zofanana ndi za chilombo choyambacho,+ chilombo choyambacho chikuona. Chinachititsa kuti dziko lapansi ndi amene akukhala mmenemo alambire chilombo choyamba chija, chimene bala lake limene chinayenera kufa nalo, linapola.+ 13 Chinachitanso zizindikiro zazikulu, moti chinapangitsa kuti moto ugwere padziko lapansi kuchokera kumwamba, anthu akuona.

14 Chilombocho chinasocheretsa anthu amene akukhala padziko lapansi chifukwa cha zizindikiro zimene chinaloledwa kuchita pamaso pa chilombo choyamba chija. Chinauzanso amene akukhala padziko lapansi kuti apange chifaniziro+ cha chilombo chimene chinali ndi bala la lupanga chija, koma sichinafe.+ 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya* kwa chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula komanso kuchititsa kuti onse amene akukana kulambira chifaniziro cha chilombocho aphedwe.

16 Chilombocho chinakakamiza anthu onse, olemekezeka ndi onyozeka, olemera ndi osauka, mfulu ndi akapolo, kuti aikidwe chizindikiro padzanja lawo lamanja kapena pachipumi pawo.+ 17 Chinachita zimenezi kuti aliyense asathe kugula kapena kugulitsa, kupatulapo ngati ali ndi chizindikirocho, dzina+ la chilombo kapena nambala ya dzina lake.+ 18 Apa mʼpamene pakufunika nzeru: Amene ali ndi nzeru awerengere nambala ya chilombocho, chifukwa ndi nambala ya munthu. Nambala yake ndi 666.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena