Davide analira Abisalomu (1-4)
Yowabu anadzudzula Davide (5-8a)
Davide anabwerera ku Yerusalemu (8b-15)
Simeyi anapempha kuti amukhululukire (16-23)
Mefiboseti anasonyeza kuti anali wosalakwa (24-30)
Barizilai analemekezedwa (31-40)
Mkangano pakati pa mafuko (41-43)