Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Ezara EZARA ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Mfumu Koresi inalamula kuti kachisi amangidwenso (1-4) Kukonzekera kuchoka ku ukapolo ku Babulo (5-11) 2 Anthu amene anabwerera kuchokera ku ukapolo (1-67) Atumiki a pakachisi (43-54) Ana a atumiki a Solomo (55-57) Zopereka zaufulu pakachisi (68-70) 3 Anamanganso guwa nʼkuperekapo nsembe (1-6) Ntchito yomanganso kachisi inayambika (7-9) Anamanga maziko a kachisi (10-13) 4 Anthu ankatsutsa ntchito yomanganso kachisi (1-6) Adani analemba kalata kwa Mfumu Aritasasita (7-16) Zomwe Aritasasita anayankha (17-22) Ntchito yomanga kachisi inaimitsidwa (23, 24) 5 Ayuda anayambiranso kumanga kachisi (1-5) Tatenai analembera kalata Mfumu Dariyo (6-17) 6 Dariyo anafufuza nʼkupereka lamulo (1-12) Kachisi anamalizidwa nʼkutseguliridwa (13-18) Anachita Pasika (19-22) 7 Ezara anapita ku Yerusalemu (1-10) Aritasasita analembera Ezara kalata (11-26) Ezara anatamanda Yehova (27, 28) 8 Anthu amene anabwerera ndi Ezara (1-14) Kukonzekera ulendo (15-30) Kunyamuka ku Babulo nʼkufika ku Yerusalemu (31-36) 9 Aisiraeli anakwatira akazi a mitundu ina (1-4) Pemphero la Ezara lovomereza machimo (5-15) 10 Pangano loti achotse akazi a mitundu ina (1-14) Akazi a mitundu ina anatumizidwa kwawo (15-44)