Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili M‘buku la Esitere ESITERE ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Phwando la Mfumu Ahasiwero ku Susani (1-9) Mfumukazi Vasiti anakana kumvera mfumu (10-12) Mfumu inafunsira malangizo kwa amuna anzeru (13-20) Mfumu inatumiza makalata (21, 22) 2 Kufufuza mfumukazi yatsopano (1-14) Esitere anakhala mfumukazi (15-20) Moredikayi anaulula chiwembu (21-23) 3 Hamani anakwezedwa ndi mfumu (1-4) Hamani anakonza chiwembu chopha Ayuda (5-15) 4 Moredikayi analira (1-5) Moredikayi anapempha Esitere kuti athandize (6-17) 5 Esitere anaonekera kwa mfumu (1-8) Hamani anasonyeza kukwiya komanso kudzikweza (9-14) 6 Moredikayi analemekezedwa ndi mfumu (1-14) 7 Esitere anaulula chiwembu cha Hamani (1-6a) Hamani anapachikidwa pamtengo umene anakonza (6b-10) 8 Moredikayi anakwezedwa (1, 2) Esitere anachonderera mfumu (3-6) Lamulo la mfumu loti Ayuda adziteteze (7-14) Ayuda anapeza mtendere ndipo anayamba kusangalala (15-17) 9 Ayuda anapambana (1-19) Anakhazikitsa chikondwerero cha Purimu (20-32) 10 Moredikayi anakhala wamphamvu (1-3)