NYIMBO YA SOLOMO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
MSULAMI ALI MUMSASA WA MFUMU SOLOMO (1:1–3:5)
-
Nyimbo yoposa nyimbo zonse (1)
Mtsikana (2-7)
Ana aakazi a ku Yerusalemu (8)
Mfumu (9-11)
“Ife tikupangira zokongoletsa zagolide” (11)
Mtsikana (12-14)
‘Wachikondi wanga ali ngati kathumba konunkhira ka mule’ (13)
Mʼbusa (15)
“Ndiwe wokongola wokondedwa wanga”
Mtsikana (16, 17)
“Iwenso ndiwe wooneka bwino, wachikondi wanga” (16)
-
MSULAMI ALI KU YERUSALEMU (3:6–8:4)
-
Ana aakazi a Ziyoni (6-11)
Gulu la anthu limene linkayenda ndi Solomo
-
MSULAMI WABWERERA KWAWO, WASONYEZA KUTI NDI WOKHULUPIRIKA (8:5-14)
-
Azichimwene ake a mtsikana (5a)
‘Kodi ndi ndani amene wakoleka dzanja mʼkhosi mwa wachikondi wake?’
Mtsikana (5b-7)
“Mofanana ndi Manda, chikondi sichigonja” (6)
Azichimwene ake a mtsikana (8, 9)
“Akakhala khoma, . . . koma akakhala chitseko, . . .” (9)
Mtsikana (10-12)
“Ine ndine khoma” (10)
Mʼbusa (13)
‘Ndikufuna ndimve mawu akoʼ
Mtsikana (14)
“Thamanga ngati insa”
-