EZEKIELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Yerusalemu ndi mtengo wa mpesa wopanda ntchito (1-8)
-
Mulungu ankakonda Yerusalemu (1-63)
Anamupeza ngati mwana wotayidwa patchire (1-7)
Mulungu anamukongoletsa nʼkupangana naye pangano la ukwati (8-14)
Anakhala wosakhulupirika (15-34)
Anapatsidwa chilango chifukwa anali mkazi wachigololo (35-43)
Anamuyerekezera ndi Samariya komanso Sodomu (44-58)
Mulungu anakumbukira pangano lake (59-63)
-
Nyimbo yoimba polira yokhudza atsogoleri a Isiraeli (1-14)
-
Nyimbo yoimba polira yokhudza sitima yapamadzi ya Turo imene ikumira (1-36)
-
Kugwa kwa Iguputo, yemwe ndi mtengo wautali wa mkungudza (1-18)
-
Ulosi wokhudza dera lamapiri la Seiri (1-15)