DANIELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-
Mfumu Nebukadinezara inalota maloto ochititsa mantha (1-4)
Anthu anzeru analephera kumasulira maloto (5-13)
Danieli anapempha Mulungu kuti amuthandize (14-18)
Anatamanda Mulungu chifukwa anawaululira chinsinsi (19-23)
Danieli anauza mfumu maloto ake (24-35)
Kumasulira maloto (36-45)
Mwala umene ukuimira Ufumu, unaphwanya chifaniziro (44, 45)
Danieli analemekezedwa ndi mfumu (46-49)
-
Fano lagolide la Mfumu Nebukadinezara (1-7)
Analamula kuti aliyense alambire fano (4-6)
Aheberi atatu anawaneneza kuti sakumvera (8-18)
“Sititumikira milungu yanu” (18)
Anaponyedwa mungʼanjo yamoto (19-23)
Anapulumutsidwa modabwitsa mungʼanjo yamoto (24-27)
Mfumu inalemekeza Mulungu wa Aheberi (28-30)