Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili Mʼbuku la Obadiya OBADIYA ZIMENE ZILI MʼBUKULI Anthu onyada a ku Edomu anachititsidwa manyazi (1-9) Anthu a ku Edomu anachitira nkhanza Yakobo (10-14) Tsiku la Yehova loweruza mitundu yonse (15, 16) Nyumba ya Yakobo idzabwezeretsedwa (17-21) Edomu adzatenthedwa ndi moto wa Yakobo (18) Yehova adzakhala Mfumu (21)