Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Zimene Zili M‘buku la Yona YONA ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Yona ankafuna kuthawa Yehova (1-3) Yehova anayambitsa chimphepo (4-6) Mavuto anayamba chifukwa cha Yona (7-13) Yona anaponyedwa mʼnyanja (14-16) Chinsomba chinameza Yona (17) 2 Pemphero la Yona ali mʼmimba mwa chinsomba (1-9) Chinsomba chinalavulira Yona kumtunda (10) 3 Yona anamvera Mulungu nʼkupita ku Nineve (1-4) Anthu a ku Nineve analapa atamva uthenga wa Yona (5-9) Mulungu anaganiza zoti asawononge Nineve (10) 4 Yona anakwiya ndipo ankafuna kufa (1-3) Yehova anaphunzitsa Yona kukhala wachifundo (4-11) “Kodi pali chifukwa choti ukwiyire choncho?” (4) Anamuphunzitsa pogwiritsa ntchito chomera chamtundu wa mphonda (6-10)